Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 23:15 - Buku Lopatulika

15 inde, ngakhale Herode yemwe; pakuti iye anambwezera Iye kwa ife; ndipo taonani, sanachite Iye kanthu kakuyenera kufa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 inde, ngakhale Herode yemwe; pakuti iye anambwezera Iye kwa ife; ndipo taonani, sanachite Iye kanthu kakuyenera kufa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Herode yemwe sadampeze mlandu, nchifukwa chake wamubweza kwa ife. Ameneyu sadachite kanthu koyenera kumuphera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Herodenso sanapeze chifukwa pakuti wamutumizanso kwa ife monga mmene mukuoneramu. Iyeyu sanachite chinthu chakuti aphedwe.

Onani mutuwo Koperani




Luka 23:15
3 Mawu Ofanana  

Ndipo akuluwa ndi akalonga anayesa kumtola chifukwa Daniele, kunena za ufumuwo; koma sanakhoze kupeza chifukwa kapena cholakwira, popeza anali wokhulupirika; ndipo saonana chosasamala kapena cholakwa chilichonse mwa iye.


Nthawi imeneyo Herode mfumu anamva mbiri ya Yesu,


Ndipo Herode anati, Yohane ndinamdula mutu ine; koma uyu ndani ndikumva zotere za iye? Ndipo anafunafuna kumuona Iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa