Luka 22:66 - Buku Lopatulika66 Ndipo pamene kunacha, bungwe la akulu a anthu linasonkhana, ndiwo ansembe aakulu ndi alembi; ndipo anapita naye kubwalo lao, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201466 Ndipo pamene kunacha, bungwe la akulu a anthu linasonkhana, ndiwo ansembe aakulu ndi alembi; ndipo anapita naye kubwalo lao, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa66 Kutacha, a m'Bungwe Lalikulu la Ayuda adasonkhana, ndiye kuti akulu a ansembe ndi aphunzitsi a Malamulo. Adatenga Yesu napita naye ku Bwalo lao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero66 Kutacha, bungwe la akuluakulu, pamodzi ndi akulu a ansembe ndi aphunzitsi amalamulo, anakumana pamodzi, ndipo anamuyika Yesu patsogolo pawo. Onani mutuwo |