Luka 22:65 - Buku Lopatulika65 Ndipo zambiri zina anamnenera Iye, namchitira mwano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201465 Ndipo zambiri zina anamnenera Iye, namchitira mwano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa65 Ndipo adamnenanso mau ena ambiri achipongwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero65 Ndipo iwo anamunena zachipongwe zambiri. Onani mutuwo |