Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 22:64 - Buku Lopatulika

64 Ndipo anamkulunga Iye m'maso, namfunsa, nati, Talota; anakupanda Iwe ndani?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

64 Ndipo anamkulunga Iye m'maso, namfunsa, nati, Talota; anakupanda Iwe ndani?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

64 Adammanga nsalu m'maso nkumamufunsa kuti, “Lota, wakumenya ndani?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

64 Anamumanga mʼmaso ndi kumufunsa kuti, “Tanenera! Wakumenya iwe ndi ndani?”

Onani mutuwo Koperani




Luka 22:64
4 Mawu Ofanana  

nati, Utilote ife, Khristu Iwe; wakumenya Iwe ndani?


Ndipo ena anayamba kumthira malovu Iye, ndi kuphimba nkhope yake, ndi kumbwanyula, ndi kunena naye, Lota; ndipo anyamatawo anampanda Iye khofu.


Pamenepo Afilisti anamgwira, namkolowola maso, natsika naye ku Gaza, nammanga ndi maunyolo amkuwa; namperetsa m'kaidi.


Ndipo kunali, pakukondwera mitima yao, anati, Kaitaneni Samisoni, atisewerere. Naitana Samisoni m'kaidi; nasewera iye pamaso pao; ndipo anamuka iye pakati pa mizati.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa