Luka 22:49 - Buku Lopatulika49 Ndipo m'mene iwo akumzinga Iye anaona chimene chiti chichitike, anati, Ambuye, tidzakantha ndi lupanga kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Ndipo m'mene iwo akumzinga Iye anaona chimene chiti chichitike, anati, Ambuye, tidzakantha ndi lupanga kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Ophunzira amene anali pafupi ndi Yesu ataona zimene zinalikudzachitika, adafunsa Yesu kuti, “Ambuye, kodi tiŵateme ndi lupanga?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Otsatira Yesu ataona zimene zimati zichitike, anati, “Ambuye, kodi timenyane ndi malupanga athu?” Onani mutuwo |