Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 22:48 - Buku Lopatulika

48 Koma Yesu anati kwa iye, Yudasi, ulikupereka Mwana wa Munthu ndi chimpsompsono kodi?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

48 Koma Yesu anati kwa iye, Yudasi, ulikupereka Mwana wa Munthu ndi chimpsompsono kodi?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

48 Koma Yesu adamufunsa kuti, “Yudasi, mongadi ukupereka Mwana wa Munthu kwa adani pakumumpsompsona?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

48 Koma Yesu anamufunsa kuti, “Yudasi, kodi ukupereka Mwana wa Munthu ndi mpsopsono?”

Onani mutuwo Koperani




Luka 22:48
7 Mawu Ofanana  

Pakamwa pake mposalala ngati mafuta amkaka, koma mumtima mwake munali nkhondo, mau ake ngofewa ngati mafuta oyenga, koma anali malupanga osololasolola.


Kulasa kwa bwenzi kuli kokhulupirika; koma mdani apsompsona kawirikawiri.


Pamene Iye anali chilankhulire, taonani, khamu la anthu, ndipo iye wotchedwa Yudasi, mmodzi wa khumi ndi awiriwo, anawatsogolera; nayandikira Yesu kumpsompsona Iye.


Ndipo m'mene iwo akumzinga Iye anaona chimene chiti chichitike, anati, Ambuye, tidzakantha ndi lupanga kodi?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa