Luka 22:46 - Buku Lopatulika46 ndipo anati kwa iwo, Mugoneranji? Ukani, pempherani kuti mungalowe m'kuyesedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201446 ndipo anati kwa iwo, Mugoneranji? Ukani, pempherani kuti mungalowe m'kuyesedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa46 ndipo adaŵafunsa kuti, “Bwanji mukugona? Dzukani ndi kumapemphera, kuti mungagwe m'zokuyesani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero46 Iye anafunsa kuti, Nʼchifukwa chiyani mukugona? “Dzukani ndipo pempherani kuti inu musagwe mʼmayesero.” Onani mutuwo |