Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 22:45 - Buku Lopatulika

45 Ndipo pamene ananyamuka pakupemphera anadza kwa ophunzira, nawapeza ali m'tulo ndi chisoni,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

45 Ndipo pamene ananyamuka pakupemphera anadza kwa ophunzira, nawapeza ali m'tulo ndi chisoni,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

45 Atapemphera, adaimirira napita kwa ophunzira ake. Adaŵapeza ali m'tulo chifukwa cha chisoni,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

45 Iye atamaliza kupemphera, ndi kubwerera kwa ophunzira ake, anawapeza atagona atafowoka ndi chisoni.

Onani mutuwo Koperani




Luka 22:45
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anadza kwa ophunzira, nawapeza iwo ali m'tulo, nanena kwa Petro, Nkutero kodi? Simungathe kuchezera ndi Ine mphindi imodzi?


Ndipo anabweranso, nawapeza iwo ali m'tulo, pakuti zikope zao zinalemera ndi tulo.


Ndipo anadza nawapeza iwo ali m'tulo, nanena ndi Petro, Simoni, ugona kodi? Unalibe mphamvu yakudikira ora limodzi kodi?


Ndipo pokhala Iye m'chipsinjo mtima anapemphera kolimba koposa ndithu: ndi thukuta lake linakhala ngati madontho aakulu a mwazi alinkugwa pansi.


ndipo anati kwa iwo, Mugoneranji? Ukani, pempherani kuti mungalowe m'kuyesedwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa