Luka 22:28 - Buku Lopatulika28 Koma inu ndinu amene munakhala ndi Ine chikhalire m'mayesero anga; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Koma inu ndinu amene munakhala ndi Ine chikhalire m'mayesero anga; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 “Inu ndinu amene mwakhala ndi Ine pa masautso anga onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Inu ndinu amene mwayima nane mʼmayesero. Onani mutuwo |