Luka 21:28 - Buku Lopatulika28 Koma poyamba kuchitika izi weramukani, tukulani mitu yanu; chifukwa chiomboledwe chanu chayandikira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Koma poyamba kuchitika izi weramukani, tukulani mitu yanu; chifukwa chiomboledwe chanu chayandikira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Zimenezi zikadzayamba kuchitika, mudzaimirire nkukweza mitu yanu, chifukwa chipulumutso chanu chayandikira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Zinthu izi zikadzayamba kuchitika, mudzayimirire ndi kutukula mitu yanu, chifukwa chipulumutso chanu chayandikira.” Onani mutuwo |