Luka 21:22 - Buku Lopatulika22 Chifukwa amenewa ndi masiku akubwezera, kuti zonse zidalembedwa zichitike. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Chifukwa amenewa ndi masiku akubwezera, kuti zonse zidalembedwa zichitike. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Chifukwa masiku amenewo adzakhala masiku akulipsira, kuti zonse zija zimene zidaalembedwa m'Malembo zipherezere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Pakuti iyi ndi nthawi yachilango pokwaniritsa zonse zimene zinalembedwa. Onani mutuwo |