Luka 20:45 - Buku Lopatulika45 Ndipo pamene anthu onse analinkumva Iye, anati kwa ophunzira, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Ndipo pamene anthu onse analinkumva Iye, anati kwa ophunzira, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Pamene anthu onse ankamvetsera zimene Yesu ankalankhula, Iye adauza ophunzira ake kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Pamene anthu onse ankamvetsera, Yesu anati kwa ophunzira ake, Onani mutuwo |