Luka 20:43 - Buku Lopatulika43 kufikira Ine ndikaika adani ako pansi pa mapazi ako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 kufikira Ine ndikaika adani ako pansi pa mapazi ako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 mpaka nditasandutsa adani ako kuti akhale ngati chopondapo mapazi ako.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 mpaka Ine nditasandutsa adani anu chopondapo mapazi anu?’ Onani mutuwo |