Luka 20:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo alembi ena anayankha nati, Mphunzitsi, mwanena bwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo alembi ena anayankha nati, Mphunzitsi, mwanena bwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Apo ena mwa aphunzitsi a Malamulo adauza Yesu kuti, “Aphunzitsi, mwanena bwino.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Ena mwa aphunzitsi amalamulo anayankha kuti, “Mwanena bwino mphunzitsi!” Onani mutuwo |