Luka 20:31 - Buku Lopatulika31 ndi wachitatu anamtenga mkaziyo; ndipo choteronso asanu ndi awiri onse, sanasiye mwana, namwalira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 ndi wachitatu anamtenga mkaziyo; ndipo choteronso asanu ndi awiri onse, sanasiye mwana, namwalira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 ndipo wachitatu nayenso adaloŵa chokolo. Onse aja asanu ndi aŵiri adachita chimodzimodzi, koma onse adamwalira osamsiyira ana mkaziyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 ndipo kenaka wachitatuyo anamukwatira iye, ndipo chimodzimodzi asanu ndi awiri aja anafa osasiya ana. Onani mutuwo |