Luka 20:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo anadza kwa Iye Asaduki ena, amene amanena kuti palibe kuuka kwa akufa; ndipo anamfunsa Iye, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo anadza kwa Iye Asaduki ena, amene amanena kuti palibe kuuka kwa akufa; ndipo anamfunsa Iye, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Asaduki ena adadza kwa Yesu. Paja iwo amati akufa sadzauka. Adamufunsa Yesu kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Ena mwa Asaduki, amene ankanena kuti kulibe kuuka kwa akufa, anabwera kwa Yesu ndi funso. Onani mutuwo |