Luka 20:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo sanakhoze kugwira mauwo pamaso pa anthu; ndipo anazizwa ndi kuyankha kwake, nakhala chete. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo sanakhoze kugwira mauwo pamaso pa anthu; ndipo anazizwa ndi kuyankha kwake, nakhala chete. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Choncho adalephera kumutapa m'kamwa pamaso pa anthu pa zimene Iye adalankhula. Iwo adathedwa nzeru ndi zimene Yesu adaayankha, nkungoti chete. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Iwo analephera kumupeza cholakwa pa zimene ankayankhula pamaso pa anthu. Ndipo pothedwa nzeru ndi yankho lake, iwo anakhala chete. Onani mutuwo |