Luka 20:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo Iye anati kwa iwo, Chifukwa chake perekani kwa Kaisara zake za Kaisara, ndi kwa Mulungu zake za Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo Iye anati kwa iwo, Chifukwa chake perekani kwa Kaisara zake za Kaisara, ndi kwa Mulungu zake za Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Iwo aja adati, “Zonse ndi za Mfumu ya ku Roma.” Apo Yesu adaŵauza kuti, “Tsono perekani kwa Mfumu zake za Mfumu, ndiponso kwa Mulungu zake za Mulungu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Iwo anayankha kuti, “Za Kaisara.” Iye anawawuza kuti, “Ndiye perekani kwa Kaisara zake za Kaisara ndi kwa Mulungu zimene ndi za Mulungu.” Onani mutuwo |