Luka 2:50 - Buku Lopatulika50 Ndipo sanadziwitse mau amene Iye analankhula nao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201450 Ndipo sanadziwitse mau amene Iye analankhula nao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa50 Koma iwo sadamvetse zimene adaŵayankhazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero50 Koma iwo sanazindikire chomwe Iye amatanthauza. Onani mutuwo |