Luka 2:24 - Buku Lopatulika24 ndi kukapereka nsembe monga mwanenedwa m'chilamulo cha Ambuye, njiwa ziwiri, kapena maunda awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 ndi kukapereka nsembe monga mwanenedwa m'chilamulo cha Ambuye, njiwa ziwiri, kapena maunda awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Adakaperekanso nsembe potsata Malamulo a Ambuye akuti, “Apereke njiŵa ziŵiri kapena maunda aŵiri.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 ndi kupereka nsembe posunga zimene zinanenedwa mulamulo la Ambuye: “Njiwa ziwiri kapena mawunda ankhunda awiri.” Onani mutuwo |