Luka 19:48 - Buku Lopatulika48 ndipo sanapeze chimene akachita; pakuti anthu onse anamlendewera Iye kuti amve. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201448 ndipo sanapeze chimene akachita; pakuti anthu onse anamlendewera Iye kuti amve. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa48 koma adaasoŵa chochita, chifukwa anthu onse ankatengeka nawo mtima mau ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero48 Komabe iwo sanathe kupeza njira ina iliyonse kuti achite izi, chifukwa anthu onse anakhulupirira mawu ake. Onani mutuwo |