Luka 19:45 - Buku Lopatulika45 Ndipo analowa mu Kachisi, nayamba kutulutsa iwo akugulitsa malonda, nanena nao, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Ndipo analowa m'Kachisi, nayamba kutulutsa iwo akugulitsa malonda, nanena nao, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Yesu adaloŵa m'Nyumba ya Mulungu, nayamba kutulutsa anthu amene ankachita malonda m'menemo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Kenaka Iye analowa mʼdera la Nyumba ya Mulungu ndi kuyamba kutulutsa kunja amene amachita malonda. Onani mutuwo |