Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 19:43 - Buku Lopatulika

43 Pakuti masiku adzakudzera, ndipo adani ako adzakuzingira linga, nadzakuzungulira iwe kwete, nadzakutsekereza ponsepo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

43 Pakuti masiku adzakudzera, ndipo adani ako adzakuzingira linga, nadzakuzungulira iwe kwete, nadzakutsekereza ponsepo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

43 Nthaŵi idzakufikira pamene adani ako adzakuzinga ndi machemba, nadzakuzungulira, nkukutsekereza ponseponse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

43 Pakuti masiku adzabwera pamene adani ako adzamanga mitumbira yankhondo nakuzungulira, nadzakutsekereza mbali zonse.

Onani mutuwo Koperani




Luka 19:43
15 Mawu Ofanana  

panali mzinda waung'ono muli anthu owerengeka; ndipo inadzako mfumu yaikulu, nawuzinga ndi nkhondo, nkumanga malinga aakulu;


Chifukwa chake atero Yehova za mfumu ya Asiriya, Iye sadzafika mu mzinda muno, ngakhale kuponyapo muvi, ngakhale kufika patsogolo pake ndi chikopa, ngakhale kuunjikirapo mulu.


Ana ako aakazi adzawapha kumunda ndi lupanga; ndipo adzakumangira nsanja, ndi kukuundira mtumbira, ndi kukuimikira chikopa.


nuuzinge, nuumangire nsanja zouzinga, nuundire nthumbira, ndi kuumangira misasa, nuuikire zogumulira pozungulira pake.


Koma mfumu inakwiya; nituma asilikali ake napululutsa ambanda aja, nitentha mzinda wao.


nanena, Ukadazindikira tsiku ili, inde iwetu zinthu za mtendere! Koma tsopano zibisika pamaso pako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa