Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 19:36 - Buku Lopatulika

36 Ndipo pakupita Iye, anayala zovala zao m'njira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Ndipo pakupita Iye, anayala zovala zao m'njira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Pamene Yesu ankapita, anthu adamchitira ulemu pakuyala zovala zao mu mseu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Pamene ankapita, anthu anayala zovala zawo mu msewu.

Onani mutuwo Koperani




Luka 19:36
4 Mawu Ofanana  

Nafulumira iwo, nagwira yense chofunda chake, nachiyala pokhala iye pachiunda, naomba lipenga, nati, Yehu ndiye mfumu.


Ndipo ambirimbiri a mpingowo anayala zovala zao panjira; ndipo ena anadula nthambi za mitengo, naziyala m'njiramo.


Ndipo anadza naye kwa Yesu; ndipo anayalika zovala zao pa mwana wa buluyo, nakwezapo Yesu.


Ndipo pakuyandikira Iye tsono potsetsereka pake paphiri la Azitona, unyinji wonse wa ophunzira anayamba kukondwera ndi kuyamika Mulungu ndi mau aakulu, chifukwa cha ntchito zonse zamphamvu anaziona;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa