Luka 19:27 - Buku Lopatulika27 Koma adani anga aja osafuna kuti ndidzakhala mfumu yao, bwerani nao kuno, nimuwaphe pamaso panga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Koma adani anga aja osafuna kuti ndidzakhala mfumu yao, bwerani nao kuno, nimuwaphe pamaso panga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Koma adani angaŵa, aja ankakana kuti ndikhale mfumu yaoŵa, bwera nawoni kuno, muŵaphe ine ndikuwona.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Tsono adani anga aja amene sankafuna kuti ndikhale mfumu yawo, abweretseni pano ndi kuwapha ine ndikuona.” Onani mutuwo |