Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 19:25 - Buku Lopatulika

25 Ndipo anati kwa iye, Mbuye, ali nazo mina khumi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndipo anati kwa iye, Mbuye, ali nazo mina khumi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 “Iwo adamuyankha kuti, ‘Pepani, ambuye, ameneyu ali kale ndi ndalama makumi khumi.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Iwo anati, “Bwana iyeyu ali nazo kale khumi!”

Onani mutuwo Koperani




Luka 19:25
5 Mawu Ofanana  

Ndipo ichinso chinali pamaso panu chinthu chaching'ono, Yehova Mulungu; koma munanenanso za banja la mnyamata wanu kufikira nthawi yaikulu ilinkudza; ndipo mwatero monga mwa machitidwe a anthu, Yehova Mulungu!


Ndipo anamuitana, nati kwa iye, Ichi ndi chiyani ndikumva za iwe? Undiwerengere za ukapitao wako; pakuti sungathe kukhalabe kapitao.


Ndipo anati kwa iwo akuimirirapo, Mchotsereni minayo, nimuipatse kwa iye wakukhala nazo mina khumi.


Ndinena ndi inu, kuti kwa yense wakukhala nacho kudzapatsidwa; koma kwa iye amene alibe kanthu, chingakhale chimene ali nacho chidzachotsedwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa