Luka 18:36 - Buku Lopatulika36 ndipo pakumva khamu la anthu alinkupita, anafunsa, Ichi nchiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 ndipo pakumva khamu la anthu alinkupita, anafunsa, Ichi nchiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Atamva anthu ambirimbiri akupita mumseumo, adafunsa kuti, “Kodi kuli chiyani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 anamva gulu la anthu likudutsa. Iye anafunsa chomwe chimachitika. Onani mutuwo |