Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 18:29 - Buku Lopatulika

29 Koma anati kwa iwo, Indetu ndinena kwa inu, Palibe munthu wasiya nyumba, kapena mkazi, kapena abale, kapena akum'bala, kapena ana, chifukwa cha Ufumu wa Mulungu,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Koma anati kwa iwo, Indetu ndinena kwa inu, Palibe munthu wasiya nyumba, kapena mkazi, kapena abale, kapena akum'bala, kapena ana, chifukwa cha Ufumu wa Mulungu,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Yesu adaŵauza kuti, “Ndithu ndikunenetsa kuti aliyense wosiya nyumba, kapena mkazi, kapena abale, kapena makolo, kapena ana chifukwa cha Ufumu wa Mulungu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Yesu anawawuza kuti, “Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti palibe amene anasiya nyumba kapena mkazi kapena abale kapena makolo kapena ana chifukwa cha ufumu wa Mulungu

Onani mutuwo Koperani




Luka 18:29
7 Mawu Ofanana  

Koma muyambe mwafuna Ufumu wake ndi chilungamo chake, ndipo zonse zimenezo zidzaonjezedwa kwa inu.


Ndipo anati wina, Ine ndakwatira mkazi, ndipo chifukwa chake sindingathe kudza.


amene anati za atate wake ndi amai wake, sindinamuone; Sanazindikire abale ake, sanadziwe ana ake omwe; popeza anasamalira mau anu, nasunga chipangano chanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa