Luka 18:26 - Buku Lopatulika26 Koma akumvawo anati, Tsono ndani angathe kupulumutsidwa? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Koma akumvawo anati, Tsono ndani angathe kupulumutsidwa? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Anthu amene adamva zimenezi adafunsa kuti, “Tsono nanga angathe kupulumuka ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Amene anamva izi anafunsa kuti, “Nanga ndani amene angapulumuke?” Onani mutuwo |