Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 18:20 - Buku Lopatulika

20 Udziwa malamulo. Usachite chigololo, Usaphe, Usabe, Usachite umboni wonama, Lemekeza atate wako ndi amai ako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Udziwa malamulo. Usachite chigololo, Usaphe, Usabe, Usachite umboni wonama, Lemekeza atate wako ndi amai ako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Malamulo ukuŵadziŵa: Usachite chigololo, usaphe, usabe, usachite umboni wonama, lemekeza atate ako ndi amai ako.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Iwe umadziwa malamulo: ‘Usachite chigololo, usaphe, usabe, usapereke umboni wonama, lemekeza abambo ndi amayi ako.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Luka 18:20
15 Mawu Ofanana  

Kuchilamulo ndi kuumboni! Ngati iwo sanena malinga ndi mau awa, ndithu sadzaona mbandakucha.


Koma Yesu anati kwa iye, Unditcha Ine wabwino bwanji? Palibe wabwino, koma mmodzi, ndiye Mulungu.


Koma anati, Izi zonse ndazisunga kuyambira ubwana wanga.


Pakuti ili, Usachite chigololo, Usaphe, Usabe, Usasirire, ndipo lingakhale lamulo lina lililonse, limangika pamodzi m'mau amenewa, kuti, Uzikonda mnzako monga udzikonda iwe wekha.


chifukwa kuti pamaso pake palibe munthu adzayesedwa wolungama ndi ntchito za lamulo; pakuti uchimo udziwika ndi lamulo.


Lemekeza atate wako ndi amai ako (ndilo lamulo loyamba lokhala nalo lonjezano),


Ana inu, mverani akubala inu m'zonse, pakuti ichi Ambuye akondwera nacho.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa