Luka 18:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo anadza nao kwa Iye ana amakanda kuti awakhudze; koma pamene ophunzira anaona anawadzudzula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo anadza nao kwa Iye ana amakanda kuti awakhudze; koma pamene ophunzira anaona anawadzudzula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Anthu ena ankabwera ndi ana omwe kwa Yesu kuti aŵakhudze. Ophunzira ake poona zimenezi, ankaŵazazira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Anthu amabweretsanso ana aangʼono kwa Yesu kuti awadalitse. Ophunzira ataona izi, anawadzudzula. Onani mutuwo |