Luka 17:35 - Buku Lopatulika35 Padzakhala akazi awiri akupera pamodzi, mmodzi adzatengedwa, ndi wina adzasiyidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Padzakhala akazi awiri akupera pamodzi, mmodzi adzatengedwa, ndi wina adzasiyidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Azimai aŵiri adzakhala akusinja pamodzi, mmodzi adzamtenga, winayo nkumusiya, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Amayi awiri adzakhala pamodzi akusinja; wina adzatengedwa ndi wina adzasiyidwa. Onani mutuwo |