Luka 17:28 - Buku Lopatulika28 Monga momwenso kunakhala masiku a Loti; anadya, anamwa, anagula, anagulitsa, anabzala, anamanga nyumba; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Monga momwenso kunakhala masiku a Loti; anadya, anamwa, anagula, anagulitsa, anabzala, anamanga nyumba; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Monga momwe zidaachitikiranso pa nthaŵi ya Loti. Anthu ankangodya ndi kumwa, ankagulitsana malonda, ankabzala mbeu, ankamanga nyumba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 “Zinalinso chimodzimodzi nthawi ya Loti. Anthu ankadya ndi kumwa, kugula ndi kugulitsa, kudzala ndi kumanga. Onani mutuwo |