Luka 14:29 - Buku Lopatulika29 Kuti kungachitike, pamene atakhazika pansi miyala ya kumaziko ake, osakhoza kuimaliza anthu onse akuyang'ana adzayamba kumseka iye, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Kuti kungachitike, pamene atakhazika pansi miyala ya kumaziko ake, osakhoza kuimaliza anthu onse akuyang'ana adzayamba kumseka iye, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Akapanda kutero, mwina adzaika maziko, nkulephera kuitsiriza. Apo anthu onse, poona zimenezi, adzayamba kumseka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Pakuti ngati ayika maziko ndi kulephera kutsiriza, aliyense amene adzayiona adzamuseka, Onani mutuwo |