Luka 14:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo aliyense amene sasenza mtanda wake wa mwini yekha, ndi kudza pambuyo panga, sangathe kukhala wophunzira wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo amene aliyense sasenza mtanda wake wa mwini yekha, ndi kudza pambuyo panga, sakhoza kukhala wophunzira wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Aliyense amene sasenza mtanda wake nkumanditsata, sangakhale wophunzira wanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Ndipo aliyense amene sasenza mtanda wake ndi kunditsata Ine sangakhale ophunzira wanga. Onani mutuwo |