Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 14:20 - Buku Lopatulika

20 Ndipo anati wina, Ine ndakwatira mkazi, ndipo chifukwa chake sindingathe kudza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndipo anati wina, Ine ndakwatira mkazi, ndipo chifukwa chake sindingathe kudza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Ndipo wina adati, ‘Ndangokwatira tsopano apa, choncho sinditha kubwera.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 “Wina anatinso, ‘Ine ndangokwatira kumene, choncho sinditha kubwera.’

Onani mutuwo Koperani




Luka 14:20
7 Mawu Ofanana  

Ndipo anati wina, Ine ndagula ng'ombe za magoli asanu, ndipo ndinka kukaziyesa; ndikupempha undilole ine ndisafika.


Ndipo kapoloyo pakubwera anauza mbuye wake zinthu izi. Pamenepo mwini nyumba anakwiya, nati kwa kapolo wake, Tuluka msanga, pita kumakwalala ndi kunjira za mzinda, nubwere nao muno aumphawi ndi opunduka ndi akhungu ndi otsimphina.


koma iye wokwatira alabadira zinthu za dziko lapansi, kuti akondweretse mkazi wake.


Munthu akatenga mkazi watsopano, asatuluke ku nkhondo, kapena asamchititse kanthu kalikonse; akhale waufulu kunyumba yake chaka chimodzi, nakondweretse mkazi adamtengayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa