Luka 14:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo anati wina, Ine ndagula ng'ombe za magoli asanu, ndipo ndinka kukaziyesa; ndikupempha undilole ine ndisafika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo anati wina, Ine ndagula ng'ombe za magoli asanu, ndipo ndinka kukaziyesa; ndikupempha undilole ine ndisafika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Wina adati, ‘Ndidagula ng'ombe khumi zapagoli, ndiye ndikukaziyesa. Pepani sindibwera.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 “Wina anati, ‘Ndangogula kumene ngʼombe khumi zokoka ngolo ndipo kupita kukaziyesa. Pepani mundikhululukire.’ Onani mutuwo |