Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 14:17 - Buku Lopatulika

17 ndipo anatumiza kapolo wake pa nthawi ya phwando kukanena kwa oitanidwawo, Idzani, chifukwa zonse zakonzeka tsopano.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 ndipo anatumiza kapolo wake pa nthawi ya phwando kukanena kwa oitanidwawo, Idzani, chifukwa zonse zakonzeka tsopano.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Nthaŵi ya phwando itakwana adatuma wantchito wake kukauza oitanidwa aja kuti, ‘Bwerani, pakuti zonse zakonzeka.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Nthawi yaphwando itakwana anatuma wantchito wake kuti akawuze onse amene anayitanidwa kuti, ‘Bwerani, pakuti zonse zakonzeka.’

Onani mutuwo Koperani




Luka 14:17
17 Mawu Ofanana  

Koma anati kwa iye, Munthu wina anakonza phwando lalikulu; naitana anthu ambiri;


Ndipo onse ndi mtima umodzi anayamba kuwiringula. Woyamba anati kwa iye, Ine ndagula munda, ndipo ndiyenera ndituluke kukauona; ndikupempha undilole ine ndisafika.


Koma tsiku lomaliza, lalikululo la chikondwerero, Yesu anaimirira nafuula, ndi kunena, Ngati pali munthu akumva ludzu, adze kwa Ine, namwe.


Amuna, abale, ana a mbadwa ya Abrahamu, ndi iwo mwa inu akuopa Mulungu, kwa ife atumidwa mau a chipulumutso ichi.


Koma zinthu zonse zichokera kwa Mulungu amene anatiyanjanitsa kwa Iye yekha mwa Khristu, natipatsa utumiki wa chiyanjanitso;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa