Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 12:49 - Buku Lopatulika

49 Ine ndinadzera kuponya moto padziko lapansi; ndipo ndifunanji ngati unatha kuyatsidwa?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

49 Ine ndinadzera kuponya moto pa dziko lapansi; ndipo ndifunanji ngati unatha kuyatsidwa?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

49 “Ndidabwera kudzaponya moto pa dziko lapansi, ndipo ndikadakonda utayaka kale.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

49 “Ine ndabwera kudzayatsa moto pa dziko lapansi, ndipo ndikanakonda ukanayaka kale.

Onani mutuwo Koperani




Luka 12:49
14 Mawu Ofanana  

koma ndi chilungamo adzaweruza aumphawi, nadzadzudzulira ofatsa a m'dziko moongoka; ndipo adzamenya dziko lapansi ndi chibonga cha kukamwa kwake, nadzapha oipa ndi mpweya wa milomo yake.


Pakuti taonani, likudza tsiku, lotentha ngati ng'anjo; ndipo onse akudzikuza ndi onse akuchita choipa. Adzakhala ngati chiputu; ndi tsiku lilinkudza lidzawayatsa, ati Yehova wa makamu, osawasiyira muzu kapena nthambi.


Koma iye amene sanachidziwe, ndipo anazichita zoyenera mikwapulo, adzakwapulidwa pang'ono. Ndipo kwa munthu aliyense adampatsa zambiri, kwa iye adzafuna zambiri; ndipo amene anamuikizira zambiri, adzamuuza abwezere zoposa.


Koma ndili ndi ubatizo ndikabatizidwe nao; ndipo ndikanikizidwa Ine kufikira ukatsirizidwa!


Tiyenera kugwira ntchito za Iye wondituma Ine, pokhala pali msana; ukudza usiku pamene palibe munthu angakhoze kugwira ntchito.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa