Luka 12:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo akadza ulonda wachiwiri, kapena wachitatu, nakawapeza atero, odala amenewa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo akadza ulonda wachiwiri, kapena wachitatu, nakawapeza atero, odala amenewa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Ngodala antchitowo mbuye waoyo akadzaŵapeza ali choncho pamene iye adzafike, ngakhale pakati pa usiku kapena kuli pafupi kucha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Zidzakhala bwino kwa antchitowo amene mbuye wawo adzawapeze ali okonzeka, ngakhale iye atabwera pa ora lachiwiri kapena lachitatu usiku. Onani mutuwo |