Luka 11:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo anazizwa Mfarisiyo, pakuona kuti anayamba chakudya asanasambe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo anazizwa Mfarisiyo, pakuona kuti anayamba chakudya asanasambe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Mfarisiyo adadabwa poona kuti Yesu wayamba kudya osatsata mwambo wao wa kasambidwe ka m'manja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Mfarisiyo anadabwa atazindikira kuti Yesu anayamba kudya wosatsata mwambo wawo wakasambidwe ka mʼmanja. Onani mutuwo |