Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 11:37 - Buku Lopatulika

37 Ndipo pakulankhula Iye, anamuitana Mfarisi kuti adye naye; ndipo analowa naseama kudya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 Ndipo pakulankhula Iye, anamuitana Mfarisi kuti adye naye; ndipo analowa naseama kudya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Pamene Yesu adatsiriza kulankhula, wina wa m'gulu la Afarisi adamuitana kuti akadye naye. Tsono Yesu adaloŵa m'nyumba nakakhala podyera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 Yesu atamaliza kuyankhula, Mfarisi wina anamuyitana kuti akadye naye. Tsono Yesu analowa mʼnyumba ndi kukhala podyera.

Onani mutuwo Koperani




Luka 11:37
5 Mawu Ofanana  

Pamenepo, ngati thupi lako lonse liunikidwa losakhala nalo dera lake lamdima, lidzakhala lounikidwa monsemo, ngati pamene nyali ndi kuwala kwake ikuunikira iwe.


Ndipo anazizwa Mfarisiyo, pakuona kuti anayamba chakudya asanasambe.


Ndipo panali pamene Iye analowa m'nyumba ya mmodzi wa akulu a Afarisi tsiku la Sabata, kukadya, iwo analikumzonda Iye.


Ndipo mmodzi wa Afarisi anamuitana Iye kuti akadye naye. Ndipo analowa m'nyumba ya Mfarisi, naseama pachakudya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa