Luka 11:33 - Buku Lopatulika33 Palibe munthu, atayatsa nyali, aiika m'chipinda chapansi, kapena pansi pa mbiya, koma pa choikapo chake, kuti iwo akulowamo aone kuunika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Palibe munthu, atayatsa nyali, aiika m'chipinda chapansi, kapena pansi pa mbiya, koma pa choikapo chake, kuti iwo akulowamo aone kuunika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 “Munthu sati akayatsa nyale, nkuiika m'chipinda chapansi kapena kuivundikira ndi mbiya. Koma amaiika pa malo oonekera, kuti anthu oloŵa m'nyumbamo aone kuŵala kwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 “Palibe amene amayatsa nyale ndi kuyiika pa malo poti sionekera, kapena pansi pa mtsuko. Mʼmalo mwake amayika pa choyikapo chake, kuti iwo amene akulowamo aone kuwunika. Onani mutuwo |