Luka 10:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo pakupita paulendo pao Iye analowa m'mudzi wina; ndipo mkazi wina dzina lake Marita anamlandira Iye kunyumba kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo pakupita paulendo pao Iye analowa m'mudzi wina; ndipo mkazi wina dzina lake Marita anamlandira Iye kunyumba kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Pamene Yesu ndi ophunzira ake anali pa ulendo wao, Iye adaloŵa m'mudzi wina. Tsono mai wina, dzina lake Marita, adamlandira kunyumba kwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Yesu ndi ophunzira ake akuyenda, anafika pa mudzi kumene mayi wotchedwa Marita anamulandira Iye mʼnyumba mwake. Onani mutuwo |