Levitiko 9:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Aroni anakweza dzanja lake kulozera anthu, nawadalitsa; natsika kuja anapereka nsembe yauchimo, ndi nsembe yopsereza, ndi nsembe zoyamika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Aroni anakweza dzanja lake kulozera anthu, nawadalitsa; natsika kuja anapereka nsembe yauchimo, ndi nsembe yopsereza, ndi nsembe zoyamika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Tsono Aroni adakweza manja ake pa Aisraele naŵadalitsa. Ndipo adatsika paguwa, pomwe adaperekera nsembe yopepesera machimo, nsembe yopsereza ndi nsembe yachiyanjano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Kenaka Aaroni anakweza manja ake pa anthuwo nawadalitsa. Ndipo atatha kupereka nsembe yopepesera machimo, nsembe yopsereza ndi nsembe yachiyanjano, anatsika pa guwapo. Onani mutuwo |