Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 9:21 - Buku Lopatulika

21 Ndipo Aroni anaweyula ngangazo ndi mwendo wathako wa ku dzanja lamanja zikhale nsembe yoweyula pamaso pa Yehova; monga Iye anauza Mose.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ndipo Aroni anaweyula ngangazo ndi mwendo wathako wa ku dzanja lamanja zikhale nsembe yoweyula pamaso pa Yehova; monga Iye anauza Mose.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Koma Aroni adaweyula ngangazo ndi ntchafu ya ku dzanja lamanja, kuti zikhale chopereka choweyula pamaso pa Chauta, monga momwe Mose adaalamulira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Koma zidale ndi ntchafu ya kumanja Aaroni anaziweyula ngati chopereka choweyula pamaso pa Yehova.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 9:21
9 Mawu Ofanana  

ndipo uike zonsezi m'manja a Aroni, ndi m'manja a ana ake aamuna; nuziweyule nsembe yoweyula pamaso pa Yehova.


Iwe ndiwe mtumiki wanga, Israele, amene ndidzalemekezedwa nawe.


Ndipo mafuta a iyo idafa yokha, ndi mafuta a iyo idajiwa ndi chilombo ayenera ntchito iliyonse, koma musamadya awa konsekonse.


Ndipo musamadya mwazi uliwonse, kapena wa mbalame, kapena wa nyama, m'nyumba zanu zonse.


ndipo anaika mafuta pa ngangazo, natentha mafutawo paguwa la nsembe.


Ndipo dzidzidzi panali pamodzi ndi mngeloyo ambirimbiri a gulu la Kumwamba, natamanda Mulungu, nanena,


akalankhula wina, alankhule ngati manenedwe a Mulungu; wina akatumikira, achite ngati mu mphamvu imene Mulungu ampatsa, kuti m'zonse Mulungu alemekezedwe mwa Yesu Khristu, amene ali nao ulemerero ndi mphamvu kunthawi za nthawi. Amen.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa