Levitiko 9:20 - Buku Lopatulika20 ndipo anaika mafuta pa ngangazo, natentha mafutawo paguwa la nsembe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 ndipo anaika mafuta pa ngangazo, natentha mafutawo pa guwa la nsembe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Anawo adaika mafuta pa nganga, ndipo Aroni adatentha mafutawo pa guwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ana a Aaroni anayika mafutawo pa zidale. Pambuyo pake Aaroni anatentha mafutawo pa guwa lansembe. Onani mutuwo |