Levitiko 9:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anabwera nayo nsembe yopsereza naipereka monga mwa lemba lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anabwera nayo nsembe yopsereza naipereka monga mwa lemba lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Apo adabwera ndi nsembe yopsereza, naipereka potsata mwambo wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Anabwera ndi nsembe yopsereza, nayipereka potsata mwambo wake. Onani mutuwo |