Levitiko 9:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo anapereka nsembe yopsereza kwa iye, chiwalochiwalo, ndi mutu wake; ndipo anazitentha paguwa la nsembe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo anapereka nsembe yopsereza kwa iye, chiwalochiwalo, ndi mutu wake; ndipo anazitentha pa guwa la nsembe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Pambuyo pake adampatsira nyama ya nsembe yopsereza yoduladula, pamodzi ndi mutu wake womwe, ndipo iye adazitentha pa guwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ana akewo anamupatsa nyama yoduladula ya nsembe yopsereza ija pamodzi ndi mutu ndipo anazitentha pa guwa. Onani mutuwo |