Levitiko 9:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anapha nsembe yopsereza; ndi ana a Aroni anapereka mwaziwo kwa iye, ndipo anauwaza paguwa la nsembe pozungulira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anapha nsembe yopsereza; ndi ana a Aroni anapereka mwaziwo kwa iye, ndipo anauwaza pa guwa la nsembe pozungulira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono adapha nyama ya nsembe yopsereza, ndipo ana ake a Aroniyo atampatsira magazi, iye adawaza magaziwo pa guwa molizungulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Kenaka anapha nsembe yopsereza. Ana a Aaroni atabwera ndi magazi kwa iye, Aaroniyo anawawaza mbali zonse za guwa. Onani mutuwo |